Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 6:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Ndichokereni pamaso panga inu nonse ochita zopweteka ena,+

      Chifukwa Yehova adzamva ndithu mawu a kulira kwanga.+

  • Salimo 26:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Ndimadana ndi mpingo wa anthu ochita zoipa,+

      Ndipo sindikhala pansi ndi anthu oipa.+

  • Salimo 139:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Inu Mulungu, zikanakhala bwino mukanapha woipa.+

      Pamenepo anthu amene ali ndi mlandu wa magazi+ akanandichokera,

  • Mateyu 7:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Koma ine ndidzawauza momveka bwino kuti: Sindikukudziwani ngakhale pang’ono!+ Chokani pamaso panga, anthu osamvera malamulo inu.+

  • 1 Akorinto 15:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Musasocheretsedwe. Kugwirizana ndi anthu oipa kumawononga makhalidwe abwino.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena