Aefeso 5:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho samalani kwambiri kuti mmene mukuyendera+ si monga anthu opanda nzeru, koma ngati anzeru. Aheberi 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho, chifukwa chakuti tili ndi mtambo wa mboni+ waukulu chonchi wotizungulira, tiyeninso tivule cholemera chilichonse+ ndi tchimo limene limatikola mosavuta lija.+ Ndipo tithamange mopirira+ mpikisano+ umene atiikirawu.+
12 Choncho, chifukwa chakuti tili ndi mtambo wa mboni+ waukulu chonchi wotizungulira, tiyeninso tivule cholemera chilichonse+ ndi tchimo limene limatikola mosavuta lija.+ Ndipo tithamange mopirira+ mpikisano+ umene atiikirawu.+