-
Ezekieli 13:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Unene kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Tsoka kwa akazi amene akusoka pamodzi zinthu zovala m’zigongono, amenenso akupanga zophimba kumutu za mitu ya anthu otalika mosiyanasiyana n’cholinga chakuti awakole mumsampha anthuwo.+ Kodi mukusaka miyoyo ya anthu anga? Kodi pochita zimenezi, mukuganiza kuti mupulumutsa miyoyo yanu?
-