Ezekieli 22:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Aneneri ako akukonza chiwembu mwa iwe.+ Iwo akukhadzula anthu+ ngati mkango wobangula umene wagwira nyama.+ Akulanda anthu chuma ndi zinthu zawo zamtengo wapatali.+ Achulukitsa akazi amasiye mmenemo.+ 2 Petulo 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ali ndi maso odzaza ndi chigololo+ komanso olephera kupewa kuchita tchimo,+ ndipo amakopa anthu apendapenda. Ali ndi mtima wophunzitsidwa kusirira mwansanje.+ Iwo ndi ana otembereredwa.+
25 Aneneri ako akukonza chiwembu mwa iwe.+ Iwo akukhadzula anthu+ ngati mkango wobangula umene wagwira nyama.+ Akulanda anthu chuma ndi zinthu zawo zamtengo wapatali.+ Achulukitsa akazi amasiye mmenemo.+
14 Ali ndi maso odzaza ndi chigololo+ komanso olephera kupewa kuchita tchimo,+ ndipo amakopa anthu apendapenda. Ali ndi mtima wophunzitsidwa kusirira mwansanje.+ Iwo ndi ana otembereredwa.+