Yeremiya 5:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Aneneri akulosera monama,+ ndipo ansembe akupondereza anthu ndi mphamvu zawo.+ Anthu anga nawonso akukonda zimenezi.+ Ndipo kodi anthu inu mudzachita chiyani pamapeto pake?”+ Yeremiya 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Pakuti aliyense wa iwo, kuyambira wamng’ono mpaka wamkulu akupeza phindu lachinyengo.+ Kuyambira mneneri mpaka wansembe, aliyense wa iwo akuchita zachinyengo.+ Hoseya 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Gulu la ansembe lakhala gulu la achifwamba.+ Iwo amachita zinthu zofanana ndi za anthu obisalira munthu panjira.+ Amapha anthu m’mphepete mwa njira ku Sekemu+ chifukwa amangokhalira kuchita khalidwe lotayirira.+
31 Aneneri akulosera monama,+ ndipo ansembe akupondereza anthu ndi mphamvu zawo.+ Anthu anga nawonso akukonda zimenezi.+ Ndipo kodi anthu inu mudzachita chiyani pamapeto pake?”+
13 “Pakuti aliyense wa iwo, kuyambira wamng’ono mpaka wamkulu akupeza phindu lachinyengo.+ Kuyambira mneneri mpaka wansembe, aliyense wa iwo akuchita zachinyengo.+
9 Gulu la ansembe lakhala gulu la achifwamba.+ Iwo amachita zinthu zofanana ndi za anthu obisalira munthu panjira.+ Amapha anthu m’mphepete mwa njira ku Sekemu+ chifukwa amangokhalira kuchita khalidwe lotayirira.+