Yobu 24:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Diso la wachigololo+ limadikira kuti mdima ugwe madzulo.+Iye amati, ‘Palibe diso limene lindione,’+Ndipo amaphimba kumaso kwake. Aroma 13:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Usiku uli pafupi kutha, usana wayandikira.+ Chotero tiyeni tivule ntchito za mdima+ ndipo tivale zida za kuwala.+ Aefeso 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 ndipo musamachite nawo+ ntchito zosapindulitsa za mu mdima.+ M’malomwake, muzidzudzula ntchitozo.+
15 Diso la wachigololo+ limadikira kuti mdima ugwe madzulo.+Iye amati, ‘Palibe diso limene lindione,’+Ndipo amaphimba kumaso kwake.
12 Usiku uli pafupi kutha, usana wayandikira.+ Chotero tiyeni tivule ntchito za mdima+ ndipo tivale zida za kuwala.+
11 ndipo musamachite nawo+ ntchito zosapindulitsa za mu mdima.+ M’malomwake, muzidzudzula ntchitozo.+