Miyambo 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti milomo ya mkazi wachilendo imakha uchi ngati chisa cha njuchi+ ndipo m’kamwa mwake ndi mosalala kuposa mafuta.+ Miyambo 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 kuti utetezedwe kwa mkazi wachilendo,+ ndiponso kwa mkazi wochokera kwina amene amalankhula mawu okopa.+
3 Pakuti milomo ya mkazi wachilendo imakha uchi ngati chisa cha njuchi+ ndipo m’kamwa mwake ndi mosalala kuposa mafuta.+
5 kuti utetezedwe kwa mkazi wachilendo,+ ndiponso kwa mkazi wochokera kwina amene amalankhula mawu okopa.+