Mateyu 10:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Zimene ndimakuuzani mu mdima, muzinene poyera, ndipo zimene mumamva anthu akunong’onezana, muzilalikire pamadenga.+ Machitidwe 20:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Komatu sindinakubisireni chilichonse chopindulitsa, ndipo sindinaleke kukuphunzitsani+ poyera komanso kunyumba+ ndi nyumba.
27 Zimene ndimakuuzani mu mdima, muzinene poyera, ndipo zimene mumamva anthu akunong’onezana, muzilalikire pamadenga.+
20 Komatu sindinakubisireni chilichonse chopindulitsa, ndipo sindinaleke kukuphunzitsani+ poyera komanso kunyumba+ ndi nyumba.