Salimo 11:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakuti Yehova ndi wolungama.+ Amakonda ntchito zolungama.+Anthu owongoka mtima ndi amene adzaona nkhope yake.+ Salimo 51:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Taonani! Mumakondwera ndi choonadi chochokera pansi pa mtima.+Ndipo mundidziwitse nzeru mumtima mwanga.+ Miyambo 15:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nsembe ya anthu oipa imam’nyansa Yehova,+ koma pemphero la anthu owongoka mtima limam’sangalatsa.+
7 Pakuti Yehova ndi wolungama.+ Amakonda ntchito zolungama.+Anthu owongoka mtima ndi amene adzaona nkhope yake.+
6 Taonani! Mumakondwera ndi choonadi chochokera pansi pa mtima.+Ndipo mundidziwitse nzeru mumtima mwanga.+