2 Samueli 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno Ahitofeli anauza Abisalomu kuti: “Ndilole chonde, ndisankhe amuna 12,000 kuti ndithamangitse Davide lero usiku.+ Salimo 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Amadikirira anthu pamalo obisika ngati mkango pamalo ake obisalapo.+Amawadikirira+ kuti atenge mokakamiza munthu wosautsika.Amakulunga wosautsika mu ukonde wake ndi kumutenga mokakamiza.+ Mika 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Anthu okhulupirika atha padziko lapansi, ndipo pakati pa anthu palibe munthu wowongoka mtima.+ Onse amadikirira anzawo kuti akhetse magazi.+ Aliyense amasaka m’bale wake ndi ukonde.+ Machitidwe 23:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kutacha, Ayuda anakonza chiwembu+ ndi kulumbira mwa kudzitemberera+ kuti sadya kapena kumwa kanthu kufikira atapha Paulo.+
17 Ndiyeno Ahitofeli anauza Abisalomu kuti: “Ndilole chonde, ndisankhe amuna 12,000 kuti ndithamangitse Davide lero usiku.+
9 Amadikirira anthu pamalo obisika ngati mkango pamalo ake obisalapo.+Amawadikirira+ kuti atenge mokakamiza munthu wosautsika.Amakulunga wosautsika mu ukonde wake ndi kumutenga mokakamiza.+
2 Anthu okhulupirika atha padziko lapansi, ndipo pakati pa anthu palibe munthu wowongoka mtima.+ Onse amadikirira anzawo kuti akhetse magazi.+ Aliyense amasaka m’bale wake ndi ukonde.+
12 Kutacha, Ayuda anakonza chiwembu+ ndi kulumbira mwa kudzitemberera+ kuti sadya kapena kumwa kanthu kufikira atapha Paulo.+