Mateyu 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Odala ndi anthu amene amabweretsa mtendere,+ chifukwa adzatchedwa ‘ana+ a Mulungu.’ Mateyu 18:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Komanso, ngati m’bale wako wachimwa, upite kukam’fotokozera cholakwacho panokha iwe ndi iyeyo.+ Ngati wakumvera, ndiye kuti wabweza m’bale wakoyo.+
15 “Komanso, ngati m’bale wako wachimwa, upite kukam’fotokozera cholakwacho panokha iwe ndi iyeyo.+ Ngati wakumvera, ndiye kuti wabweza m’bale wakoyo.+