Aroma 12:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ngati ndi kotheka, khalani mwamtendere+ ndi anthu onse, monga mmene mungathere. Aheberi 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yesetsani kukhala pa mtendere ndi anthu onse,+ komanso yesetsani kukhala oyera+ chifukwa ngati munthu si woyera, sadzaona Ambuye.+ Yakobo 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Komanso, chilungamo+ ndicho chipatso+ cha mbewu zimene anthu odzetsa mtendere+ amafesa mu mtendere.+
14 Yesetsani kukhala pa mtendere ndi anthu onse,+ komanso yesetsani kukhala oyera+ chifukwa ngati munthu si woyera, sadzaona Ambuye.+
18 Komanso, chilungamo+ ndicho chipatso+ cha mbewu zimene anthu odzetsa mtendere+ amafesa mu mtendere.+