1 Samueli 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Musalankhule modzikweza kwambiri anthu inu,Pakamwa panu pasatuluke mawu odzikuza,+Pakuti Yehova ndi Mulungu wodziwa zonse.+Ndipo zochita za anthu, iye amaziyeza molondola.+ 2 Petulo 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pakuti amalankhula mawu odzitukumula opanda pake, ndipo pogwiritsa ntchito zilakolako za thupi+ komanso makhalidwe otayirira, amakopa+ amene akungopulumuka+ kumene kwa anthu ochita zolakwa.
3 Musalankhule modzikweza kwambiri anthu inu,Pakamwa panu pasatuluke mawu odzikuza,+Pakuti Yehova ndi Mulungu wodziwa zonse.+Ndipo zochita za anthu, iye amaziyeza molondola.+
18 Pakuti amalankhula mawu odzitukumula opanda pake, ndipo pogwiritsa ntchito zilakolako za thupi+ komanso makhalidwe otayirira, amakopa+ amene akungopulumuka+ kumene kwa anthu ochita zolakwa.