Esitere 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma Hamani anaugwira mtima ndipo analowa m’nyumba yake. Kenako anatumiza uthenga kuti anzake ndi mkazi wake Zeresi+ abwere. Miyambo 19:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chuma chimachulukitsa mabwenzi,+ koma munthu wonyozeka amalekanitsidwa ngakhale kwa bwenzi lake.+
10 Koma Hamani anaugwira mtima ndipo analowa m’nyumba yake. Kenako anatumiza uthenga kuti anzake ndi mkazi wake Zeresi+ abwere.