Genesis 24:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 n’kunena kuti: “Atamandike Yehova,+ Mulungu wa mbuyanga Abulahamu, amene sanasiye kusonyeza mbuyanga kukoma mtima kosatha ndi kukhala wokhulupirika kwa iye. Pa ulendo wangawu, Yehova wanditsogolera kunyumba kwa abale a mbuyanga.”+ Yobu 42:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano Yehova anathetsa masautso a Yobu+ pamene iye anapempherera anzake aja.+ Kuwonjezera pamenepo Yehova anayamba kum’patsa Yobu zonse zimene anali nazo, kuwirikiza kawiri.+ Salimo 25:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 M’njira zonse za Yehova muli kukoma mtima kosatha ndi choonadiKwa anthu osunga pangano+ lake ndi zikumbutso zake.+
27 n’kunena kuti: “Atamandike Yehova,+ Mulungu wa mbuyanga Abulahamu, amene sanasiye kusonyeza mbuyanga kukoma mtima kosatha ndi kukhala wokhulupirika kwa iye. Pa ulendo wangawu, Yehova wanditsogolera kunyumba kwa abale a mbuyanga.”+
10 Tsopano Yehova anathetsa masautso a Yobu+ pamene iye anapempherera anzake aja.+ Kuwonjezera pamenepo Yehova anayamba kum’patsa Yobu zonse zimene anali nazo, kuwirikiza kawiri.+
10 M’njira zonse za Yehova muli kukoma mtima kosatha ndi choonadiKwa anthu osunga pangano+ lake ndi zikumbutso zake.+