Miyambo 26:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Chidani chimaphimbidwa ndi chinyengo. Zoipa zake zidzaululika mumpingo.+ Luka 7:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Tsopano Mfarisi wina anaumiriza Yesu kuti akadye naye. Choncho anapita kunyumba+ ya Mfarisiyo ndipo anamupatsa chakudya.
36 Tsopano Mfarisi wina anaumiriza Yesu kuti akadye naye. Choncho anapita kunyumba+ ya Mfarisiyo ndipo anamupatsa chakudya.