Mateyu 26:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pamene Yesu anali ku Betaniya+ m’nyumba ya Simoni wakhate,+ Luka 11:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Atalankhula zimenezi, Mfarisi wina anam’pempha kuti akadye naye.+ Choncho iye anapitadi kukadya chakudya.
37 Atalankhula zimenezi, Mfarisi wina anam’pempha kuti akadye naye.+ Choncho iye anapitadi kukadya chakudya.