Luka 7:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Tsopano Mfarisi wina anaumiriza Yesu kuti akadye naye. Choncho anapita kunyumba+ ya Mfarisiyo ndipo anamupatsa chakudya. Luka 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kanthawi kena atalowa m’nyumba ya mmodzi wa akuluakulu a Afarisi pa sabata kukadya chakudya,+ Afarisiwo anali kumuyang’anitsitsa.+
36 Tsopano Mfarisi wina anaumiriza Yesu kuti akadye naye. Choncho anapita kunyumba+ ya Mfarisiyo ndipo anamupatsa chakudya.
14 Kanthawi kena atalowa m’nyumba ya mmodzi wa akuluakulu a Afarisi pa sabata kukadya chakudya,+ Afarisiwo anali kumuyang’anitsitsa.+