Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 50:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Iwe umadana ndi malangizo,*+

      Ndipo umaponya mawu anga kunkhongo.+

  • Miyambo 5:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Pa nthawiyo udzanena kuti: “Ndinkadana ndi malangizo* ine,+ ndipo mtima wanga sunkavomereza kudzudzula.+

  • Miyambo 13:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Munthu wonyalanyaza malangizo amasauka ndipo amadzichotsera ulemu.+ Koma amene amamvera chidzudzulo ndi amene amalemekezedwa.+

  • Aheberi 12:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Samalani kuti musasiye kumvetsera wolankhulayo.+ Pakuti ngati amene analephera kumvera wopereka chenjezo la Mulungu padziko lapansi sanapulumuke,+ kuli bwanji ifeyo? Nafenso sitidzapulumuka tikachoka kwa iye amene amalankhula ali kumwamba.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena