2 Samueli 16:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ponyoza, Simeyi anali kunena kuti: “Choka, choka, munthu wa mlandu wamagazi+ ndi wopanda pake iwe!+ Yobu 34:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kodi munthu anganene kwa mfumu kuti, ‘Ndinu wopanda pake’?Kapena angauze anthu olemekezeka kuti, ‘Ndinu oipa’?+
7 Ponyoza, Simeyi anali kunena kuti: “Choka, choka, munthu wa mlandu wamagazi+ ndi wopanda pake iwe!+
18 Kodi munthu anganene kwa mfumu kuti, ‘Ndinu wopanda pake’?Kapena angauze anthu olemekezeka kuti, ‘Ndinu oipa’?+