-
Luka 15:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 “Kapena ndi mayi uti amene atakhala ndi ndalama zokwana madalakima 10, imodzi n’kumutayika, sangayatse nyale ndi kusesa m’nyumba n’kuifufuza mosamala mpaka ataipeza?
-