Salimo 39:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Zoonadi, munthu amayenda ngati chithunzithunzi.+Ndithudi, anthu amapokosera pachabe.+Munthu amaunjika zinthu ndipo sadziwa amene adzazitute.+ Luka 12:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndipo ndidzauza+ moyo wanga kuti: “Moyo wangawe, uli ndi zinthu zambiri zabwino mwakuti zisungika kwa zaka zambiri. Ungoti phee tsopano, ndipo udye, umwe ndi kusangalala.”’+
6 Zoonadi, munthu amayenda ngati chithunzithunzi.+Ndithudi, anthu amapokosera pachabe.+Munthu amaunjika zinthu ndipo sadziwa amene adzazitute.+
19 Ndipo ndidzauza+ moyo wanga kuti: “Moyo wangawe, uli ndi zinthu zambiri zabwino mwakuti zisungika kwa zaka zambiri. Ungoti phee tsopano, ndipo udye, umwe ndi kusangalala.”’+