Genesis 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako, Yehova Mulungu anaumba munthu kuchokera kufumbi lapansi,+ ndipo anauzira mpweya wa moyo+ m’mphuno mwake, munthuyo n’kukhala wamoyo.+ Salimo 49:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti amaona kuti ngakhale anthu anzeru amafa,+Wopusa ndi wopanda nzeru, onsewo amawonongeka,+Ndipo chuma chawo amasiyira anthu ena.+
7 Kenako, Yehova Mulungu anaumba munthu kuchokera kufumbi lapansi,+ ndipo anauzira mpweya wa moyo+ m’mphuno mwake, munthuyo n’kukhala wamoyo.+
10 Pakuti amaona kuti ngakhale anthu anzeru amafa,+Wopusa ndi wopanda nzeru, onsewo amawonongeka,+Ndipo chuma chawo amasiyira anthu ena.+