Luka 9:62 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 62 Yesu anamuuza kuti: “Aliyense wogwira pulawo+ koma n’kumayang’ana zinthu za m’mbuyo+ sayenera ufumu wa Mulungu.” Afilipi 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Abale, ine sindidziyesa ngati ndalandira kale mphotoyo ayi. Koma pali chinthu chimodzi chimene ndikuchita: Ndikuiwala zinthu zakumbuyo+ ndipo ndikuyesetsa kuti ndikapeze zakutsogolo.+
62 Yesu anamuuza kuti: “Aliyense wogwira pulawo+ koma n’kumayang’ana zinthu za m’mbuyo+ sayenera ufumu wa Mulungu.”
13 Abale, ine sindidziyesa ngati ndalandira kale mphotoyo ayi. Koma pali chinthu chimodzi chimene ndikuchita: Ndikuiwala zinthu zakumbuyo+ ndipo ndikuyesetsa kuti ndikapeze zakutsogolo.+