1 Akorinto 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kapena kodi mawu amenewo kwenikweni akunenera ife? Ndithudi, mawu amenewo analembera ife,+ chifukwa wolima ayenera kulima ndi chiyembekezo ndipo munthu wopuntha mbewu azipuntha ndi chiyembekezo chodzadya nawo.+ 1 Akorinto 9:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kodi simukudziwa kuti ochita mpikisano wa liwiro+ amathamanga onse, koma mmodzi yekha ndiye amalandira mphoto?+ Thamangani+ m’njira yoti mukalandire mphotoyo.+
10 Kapena kodi mawu amenewo kwenikweni akunenera ife? Ndithudi, mawu amenewo analembera ife,+ chifukwa wolima ayenera kulima ndi chiyembekezo ndipo munthu wopuntha mbewu azipuntha ndi chiyembekezo chodzadya nawo.+
24 Kodi simukudziwa kuti ochita mpikisano wa liwiro+ amathamanga onse, koma mmodzi yekha ndiye amalandira mphoto?+ Thamangani+ m’njira yoti mukalandire mphotoyo.+