Salimo 51:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Taonani! Mumakondwera ndi choonadi chochokera pansi pa mtima.+Ndipo mundidziwitse nzeru mumtima mwanga.+ Miyambo 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 ukamazifunafuna ngati siliva,+ ndi kuzifufuza ngati chuma chobisika,+ Mlaliki 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndinapereka mtima wanga kuti udziwe nzeru ndiponso misala,+ ndipo ndadziwa uchitsiru.+ Pochita zimenezi ndazindikira kuti zimenezinso zili ngati kuthamangitsa mphepo.+
6 Taonani! Mumakondwera ndi choonadi chochokera pansi pa mtima.+Ndipo mundidziwitse nzeru mumtima mwanga.+
17 Ndinapereka mtima wanga kuti udziwe nzeru ndiponso misala,+ ndipo ndadziwa uchitsiru.+ Pochita zimenezi ndazindikira kuti zimenezinso zili ngati kuthamangitsa mphepo.+