Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mlaliki 2:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ndinafufuza ndi mtima wanga wonse kuti ndidziwe uchitsiru posangalatsa thupi langa ndi vinyo,+ pamene ndinali kutsogolera mtima wanga ndi nzeru.+ Ndinachita zimenezi kuti ndione ubwino umene ana a anthu amapeza pa zimene amachita padziko lapansi pano masiku onse a moyo wawo.+

  • Mlaliki 7:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Ineyo ndinaganiziranso mumtima mwanga+ kuti ndidziwe, ndifufuze, ndiponso ndifunefune nzeru.+ Ndinafunanso kudziwa zimene zimayambitsa zinthu,+ ndiponso kudziwa kuipa kwa kupusa ndi uchitsiru wa misala.+

  • Mlaliki 10:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ntchentche zakufa n’zimene zimachititsa mafuta onunkhira oyengedwa bwino+ kuwola ndi kuyamba kununkha. Momwemonso uchitsiru pang’ono umawononga mbiri ya munthu amene akulemekezedwa chifukwa cha nzeru ndi ulemerero wake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena