Yobu 38:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Takokera chovala chako n’kuchimanga m’chiuno ngati mwamuna wamphamvu.Ndikufuna ndikufunse mafunso ndipo iweyo undiyankhe.+ Yobu 42:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Ndadziwa kuti inu mumatha kuchita zinthu zonse,+Ndipo palibe zimene simungakwanitse.+
3 Takokera chovala chako n’kuchimanga m’chiuno ngati mwamuna wamphamvu.Ndikufuna ndikufunse mafunso ndipo iweyo undiyankhe.+