Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mlaliki 2:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ineyo ndinaganizaganiza kuti nzeru n’chiyani,+ misala n’chiyani, ndipo uchitsiru n’chiyani.+ Kodi munthu wochokera kufumbi amene wabwera pambuyo pa mfumu angachite chiyani? Zimene angachite n’zimene anthu ena anachita kale.

  • Mlaliki 9:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Chimene chimamvetsa chisoni pa zinthu zonse zimene zimachitika padziko lapansi pano n’chakuti, popeza mapeto a anthu onse ndi amodzi,+ mtima wa ana a anthu ndi wodzazanso ndi zoipa.+ Mumtima mwawo mumakhala misala+ pa nthawi imene ali ndi moyo ndipo pamapeto pake, iwo amapita kwa akufa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena