Mlaliki 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndinapereka mtima wanga kuti udziwe nzeru ndiponso misala,+ ndipo ndadziwa uchitsiru.+ Pochita zimenezi ndazindikira kuti zimenezinso zili ngati kuthamangitsa mphepo.+ Mlaliki 7:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ineyo ndinaganiziranso mumtima mwanga+ kuti ndidziwe, ndifufuze, ndiponso ndifunefune nzeru.+ Ndinafunanso kudziwa zimene zimayambitsa zinthu,+ ndiponso kudziwa kuipa kwa kupusa ndi uchitsiru wa misala.+
17 Ndinapereka mtima wanga kuti udziwe nzeru ndiponso misala,+ ndipo ndadziwa uchitsiru.+ Pochita zimenezi ndazindikira kuti zimenezinso zili ngati kuthamangitsa mphepo.+
25 Ineyo ndinaganiziranso mumtima mwanga+ kuti ndidziwe, ndifufuze, ndiponso ndifunefune nzeru.+ Ndinafunanso kudziwa zimene zimayambitsa zinthu,+ ndiponso kudziwa kuipa kwa kupusa ndi uchitsiru wa misala.+