Oweruza 16:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Chotero Afilisiti anam’gwira ndi kum’boola maso+ n’kupita naye ku Gaza.+ Anam’manga ndi zomangira ziwiri zamkuwa,+ ndipo anakhala woyendetsa mwala wa mphero+ m’ndende.+ Miyambo 7:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mwadzidzidzi mnyamatayo wayamba kulondola mkaziyo+ ngati ng’ombe yamphongo yopita kokaphedwa, ndiponso ngati kuti wamangidwa m’matangadza kuti alandire chilango* cha munthu wopusa.
21 Chotero Afilisiti anam’gwira ndi kum’boola maso+ n’kupita naye ku Gaza.+ Anam’manga ndi zomangira ziwiri zamkuwa,+ ndipo anakhala woyendetsa mwala wa mphero+ m’ndende.+
22 Mwadzidzidzi mnyamatayo wayamba kulondola mkaziyo+ ngati ng’ombe yamphongo yopita kokaphedwa, ndiponso ngati kuti wamangidwa m’matangadza kuti alandire chilango* cha munthu wopusa.