Miyambo 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 N’chifukwa chake mosayembekezeka ndinagwera m’zinthu zoipa zamtundu uliwonse,+ ndipo ndinachita manyazi pamaso pa mpingo wonse.”+ Miyambo 7:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iye akulondola mkaziyo mpaka muvi utaboola chiwindi* chake,+ ngati mbalame yothamangira kumsampha,+ ndipo iye sakudziwa kuti zikukhudza moyo wake.+ Miyambo 7:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pakuti mkaziyo waphetsa anthu ambiri,+ ndipo onse amene aphedwa ndi iye ndi ochuluka.+ Miyambo 22:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pakamwa pa akazi achilendo pali ngati dzenje lakuya.+ Wotsutsidwa ndi Yehova adzagweramo.+
14 N’chifukwa chake mosayembekezeka ndinagwera m’zinthu zoipa zamtundu uliwonse,+ ndipo ndinachita manyazi pamaso pa mpingo wonse.”+
23 Iye akulondola mkaziyo mpaka muvi utaboola chiwindi* chake,+ ngati mbalame yothamangira kumsampha,+ ndipo iye sakudziwa kuti zikukhudza moyo wake.+