Salimo 37:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Khala chete pamaso pa Yehova,+Ndipo umuyembekezere ndi mtima wako wonse.+Usapse mtima ndi aliyense amene zinthu zikumuyendera bwino,+Munthu amene akukwaniritsa zolinga zake zoipa.+ Salimo 73:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Onani! Awa ndi anthu oipa, amene akukhala mosatekeseka mpaka kalekale.+Iwo achulukitsa chuma chawo.+ Malaki 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Panopa anthu odzikuza tikuwatcha odala.+ Komanso anthu ochita zoipa zinthu zikuwayendera bwino.+ Iwo ayesa Mulungu koma sakulandira chilango.’”+
7 Khala chete pamaso pa Yehova,+Ndipo umuyembekezere ndi mtima wako wonse.+Usapse mtima ndi aliyense amene zinthu zikumuyendera bwino,+Munthu amene akukwaniritsa zolinga zake zoipa.+
12 Onani! Awa ndi anthu oipa, amene akukhala mosatekeseka mpaka kalekale.+Iwo achulukitsa chuma chawo.+
15 Panopa anthu odzikuza tikuwatcha odala.+ Komanso anthu ochita zoipa zinthu zikuwayendera bwino.+ Iwo ayesa Mulungu koma sakulandira chilango.’”+