Mlaliki 7:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Zimene zinachitika kale n’zapatali ndiponso n’zozama kwambiri. Ndani angazimvetse?+ Mlaliki 11:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Monga momwe sudziwira mmene mzimu umagwirira ntchito m’thupi la mwana amene ali m’mimba mwa mayi ake,+ momwemonso sudziwa ntchito ya Mulungu woona, amene amachita zinthu zonse.+ Danieli 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iye anandiyankha kuti: “Pita Danieli, pakuti mawuwa asungidwa mwachinsinsi ndipo atsekedwa ndi kumatidwa kufikira nthawi yamapeto.+
5 Monga momwe sudziwira mmene mzimu umagwirira ntchito m’thupi la mwana amene ali m’mimba mwa mayi ake,+ momwemonso sudziwa ntchito ya Mulungu woona, amene amachita zinthu zonse.+
9 Iye anandiyankha kuti: “Pita Danieli, pakuti mawuwa asungidwa mwachinsinsi ndipo atsekedwa ndi kumatidwa kufikira nthawi yamapeto.+