2 Mbiri 35:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Atumiki akewo anamutsitsa m’galetalo n’kumukweza m’galeta lake lachiwiri lankhondo, n’kupita naye ku Yerusalemu.+ Choncho iye anafa+ ndipo anamuika m’manda a makolo ake.+ Ayuda onse ndi anthu onse okhala ku Yerusalemu anamulira+ Yosiya. Miyambo 30:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Mkango, umene ndi wamphamvu kwambiri panyama zonse zakutchire ndiponso umene suopa chilichonse n’kubwerera m’mbuyo,+
24 Atumiki akewo anamutsitsa m’galetalo n’kumukweza m’galeta lake lachiwiri lankhondo, n’kupita naye ku Yerusalemu.+ Choncho iye anafa+ ndipo anamuika m’manda a makolo ake.+ Ayuda onse ndi anthu onse okhala ku Yerusalemu anamulira+ Yosiya.
30 Mkango, umene ndi wamphamvu kwambiri panyama zonse zakutchire ndiponso umene suopa chilichonse n’kubwerera m’mbuyo,+