2 Samueli 20:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Anthuwo anafika ndi kumuzungulira ali mumzinda+ wa Abele wa ku Beti-maaka. Iwo anamanga chiunda chomenyerapo nkhondo* ndi mzindawo. Anthu onse amene anali ndi Yowabu anali kukumba pansi pa mpandawo kuti augwetse.
15 Anthuwo anafika ndi kumuzungulira ali mumzinda+ wa Abele wa ku Beti-maaka. Iwo anamanga chiunda chomenyerapo nkhondo* ndi mzindawo. Anthu onse amene anali ndi Yowabu anali kukumba pansi pa mpandawo kuti augwetse.