Mlaliki 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Panali mzinda winawake waung’ono ndipo mumzindamo munali amuna ochepa. Kenako kunabwera mfumu yamphamvu ndipo inazungulira mzindawo, n’kuunjika milu ikuluikulu yadothi yoti imenyerepo nkhondo.+ Yeremiya 33:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Pakuti Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena mawu okhudza nyumba za mumzinda uwu ndiponso okhudza nyumba za mafumu a Yuda zimene zagwetsedwa podziteteza ku ziunda zomenyerapo nkhondo ndiponso ku lupanga la adani.+ Luka 19:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Chifukwa masiku adzakufikira pamene adani ako adzamanga mpanda+ wazisonga+ kukuzungulira.+ Adaniwo adzakutsekereza ndi kukusautsa+ kuchokera kumbali zonse.
14 Panali mzinda winawake waung’ono ndipo mumzindamo munali amuna ochepa. Kenako kunabwera mfumu yamphamvu ndipo inazungulira mzindawo, n’kuunjika milu ikuluikulu yadothi yoti imenyerepo nkhondo.+
4 “Pakuti Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena mawu okhudza nyumba za mumzinda uwu ndiponso okhudza nyumba za mafumu a Yuda zimene zagwetsedwa podziteteza ku ziunda zomenyerapo nkhondo ndiponso ku lupanga la adani.+
43 Chifukwa masiku adzakufikira pamene adani ako adzamanga mpanda+ wazisonga+ kukuzungulira.+ Adaniwo adzakutsekereza ndi kukusautsa+ kuchokera kumbali zonse.