Miyambo 14:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ngakhale pamene munthu akuseka, mtima wake ukhoza kukhala ukupweteka.+ Ndipo kusangalala kumathera m’chisoni.+ Mlaliki 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti kuseka kwa anthu opusa+ kumamveka ngati kuthetheka kwa minga zomwe zikuyaka pansi pa mphika. Izinso n’zachabechabe.
13 Ngakhale pamene munthu akuseka, mtima wake ukhoza kukhala ukupweteka.+ Ndipo kusangalala kumathera m’chisoni.+
6 Pakuti kuseka kwa anthu opusa+ kumamveka ngati kuthetheka kwa minga zomwe zikuyaka pansi pa mphika. Izinso n’zachabechabe.