Mlaliki 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndi bwino kupita kunyumba yamaliro kusiyana ndi kupita kunyumba yamadyerero,+ chifukwa amenewo ndiwo mapeto a anthu onse. Chotero munthu amene ali moyo aziganizira zimenezi mumtima mwake. Mlaliki 7:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mtima wa anthu anzeru umakhala m’nyumba yamaliro,+ koma mtima wa anthu opusa umakhala m’nyumba yachisangalalo.+
2 Ndi bwino kupita kunyumba yamaliro kusiyana ndi kupita kunyumba yamadyerero,+ chifukwa amenewo ndiwo mapeto a anthu onse. Chotero munthu amene ali moyo aziganizira zimenezi mumtima mwake.
4 Mtima wa anthu anzeru umakhala m’nyumba yamaliro,+ koma mtima wa anthu opusa umakhala m’nyumba yachisangalalo.+