Mlaliki 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pakuti nzeru zimateteza+ monga mmene ndalama zimatetezera,+ koma ubwino wa kudziwa zinthu ndi wakuti nzeru zimasunga moyo wa eni nzeruzo.+ Luka 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Nanunso ndikukuuzani kuti, Dzipezereni mabwenzi+ ndi chuma chosalungama,+ kuti chumacho chikatha, akakulandireni m’malo okhala amuyaya.+
12 Pakuti nzeru zimateteza+ monga mmene ndalama zimatetezera,+ koma ubwino wa kudziwa zinthu ndi wakuti nzeru zimasunga moyo wa eni nzeruzo.+
9 “Nanunso ndikukuuzani kuti, Dzipezereni mabwenzi+ ndi chuma chosalungama,+ kuti chumacho chikatha, akakulandireni m’malo okhala amuyaya.+