Miyambo 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Munthu akagwiritsitsa nzeru, zidzakhala ngati mtengo wa moyo+ kwa iye, ndipo ozigwiritsitsa+ adzatchedwa odala.+ Miyambo 8:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Pakuti wondipeza ine, ndithu adzapezanso moyo+ ndipo Yehova adzasangalala naye,+ Miyambo 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti ine ndidzachititsa kuti masiku ako akhale ambiri+ ndipo zaka za moyo wako zidzawonjezeredwa.+
18 Munthu akagwiritsitsa nzeru, zidzakhala ngati mtengo wa moyo+ kwa iye, ndipo ozigwiritsitsa+ adzatchedwa odala.+
11 Pakuti ine ndidzachititsa kuti masiku ako akhale ambiri+ ndipo zaka za moyo wako zidzawonjezeredwa.+