Afilipi 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Muchite zimenezi pamene mukupitirizabe kugwira mwamphamvu mawu amoyo,+ kuti ndikakhale ndi chifukwa chosangalalira m’tsiku la Khristu,+ poona kuti sindinathamange pachabe, kapena kuchita khama pachabe.+
16 Muchite zimenezi pamene mukupitirizabe kugwira mwamphamvu mawu amoyo,+ kuti ndikakhale ndi chifukwa chosangalalira m’tsiku la Khristu,+ poona kuti sindinathamange pachabe, kapena kuchita khama pachabe.+