Mlaliki 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Wosonkhanitsa anthu wanena kuti: “Zachabechabe!+ Zinthu zonse n’zachabechabe!”+ Mlaliki 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho ndinaona ntchito zonse zimene zinachitidwa padziko lapansi pano,+ ndipo ndinapeza kuti zonse ndi zachabechabe ndiponso zili ngati kuthamangitsa mphepo.+
14 Choncho ndinaona ntchito zonse zimene zinachitidwa padziko lapansi pano,+ ndipo ndinapeza kuti zonse ndi zachabechabe ndiponso zili ngati kuthamangitsa mphepo.+