Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 39:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Zoonadi, munthu amayenda ngati chithunzithunzi.+

      Ndithudi, anthu amapokosera pachabe.+

      Munthu amaunjika zinthu ndipo sadziwa amene adzazitute.+

  • Mlaliki 2:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Ineyo ndinadana ndi ntchito yonse yovuta imene ndinali kugwira padziko lapansi pano,+ imene ndidzasiyire munthu amene akubwera pambuyo panga.+

  • Mlaliki 8:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Zonsezi ndaziona ndipo mtima wanga unaganizira za ntchito iliyonse imene yachitidwa padziko lapansi pano, pa nthawi imene munthu wapweteka munthu mnzake pomulamulira.+

  • Mlaliki 9:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Chimene chimamvetsa chisoni pa zinthu zonse zimene zimachitika padziko lapansi pano n’chakuti, popeza mapeto a anthu onse ndi amodzi,+ mtima wa ana a anthu ndi wodzazanso ndi zoipa.+ Mumtima mwawo mumakhala misala+ pa nthawi imene ali ndi moyo ndipo pamapeto pake, iwo amapita kwa akufa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena