Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 3:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Kwa mkaziyo, Mulungu ananena kuti: “Ndidzawonjezera kuvutika kwako pamene uli ndi pakati.+ Pobereka ana udzamva zowawa.+ Udzakhumba mwamuna wako, ndipo iye adzakulamulira.”+

  • Ekisodo 1:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Iwo anasautsa moyo wa Aisiraeliwo powagwiritsa ntchito yowawa yaukapolo, yomwe inali yoponda matope+ ndi kuumba njerwa.* Anawagwiritsa ntchito yaukapolo wa mtundu uliwonse m’munda,+ ndi ukapolo wa mtundu uliwonse umene anatha kuwagwiritsa ntchito mwankhanza.+

  • 2 Mafumu 25:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Iwo anapha ana a Zedekiya iye akuona,+ kenako Zedekiyayo anam’chititsa khungu.+ Atatero anamumanga ndi maunyolo amkuwa+ n’kupita naye ku Babulo.+

  • Mika 7:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Manja awo amachita zoipa ndipo amazichita bwino kwambiri.+ Kalonga amalamula kuti amupatse mphatso, ndipo woweruza amalandira chiphuphu poweruza.+ Munthu wotchuka amangolankhula zolakalaka za mtima wake+ ndipo onsewa amakonzera limodzi chiwembu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena