Ekisodo 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Anthu amenewa musawapezerenso udzu woumbira njerwa+ ngati kale. Muwasiye azikafuna okha udzu umenewo. Salimo 81:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mulungu akuti: “Ndinachotsa goli paphewa lake.+Manja ake anamasuka ndipo sananyamule dengu.+
7 “Anthu amenewa musawapezerenso udzu woumbira njerwa+ ngati kale. Muwasiye azikafuna okha udzu umenewo.