Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 11:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Kenako anauzana kuti: “Tiyeni tiumbe njerwa tiziotche.” Atatero, anayamba kumanga ndi njerwa, n’kumagwiritsa ntchito phula ngati matope omangira.+

  • Ekisodo 1:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Iwo anasautsa moyo wa Aisiraeliwo powagwiritsa ntchito yowawa yaukapolo, yomwe inali yoponda matope+ ndi kuumba njerwa.* Anawagwiritsa ntchito yaukapolo wa mtundu uliwonse m’munda,+ ndi ukapolo wa mtundu uliwonse umene anatha kuwagwiritsa ntchito mwankhanza.+

  • Nahumu 3:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Tunga madzi kuti upange chiunda chomenyerapo nkhondo.*+ Limbitsa malo ako okhala ndi mpanda wolimba kwambiri.+ Lowa m’matope ndi kupondaponda dothi. Gwira chikombole.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena