Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mlaliki 2:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndinachita zinthu zikuluzikulu.+ Ndinadzimangira nyumba zambirimbiri.+ Ndinalima minda ya mpesa yambirimbiri.+

  • Mlaliki 5:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Chinthu chabwino kwambiri ndiponso chokongola chimene ine ndaona, n’chakuti munthu ayenera kudya, kumwa ndi kusangalala, chifukwa cha ntchito yake yonse yovuta+ imene amaigwira mwakhama padziko lapansi pano, kwa masiku onse a moyo wake amene Mulungu woona wam’patsa. Pakuti imeneyo ndiyo mphoto yake.

  • Mlaliki 9:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Sangalala ndi moyo limodzi ndi mkazi wako amene umamukonda+ masiku onse a moyo wako wachabechabe, amene Mulungu wakupatsa padziko lapansi pano. Usangalale masiku ako onse achabechabe, pakuti imeneyo ndiyo mphoto yako pamoyo,+ ndi pa ntchito yovuta imene ukuigwira mwakhama padziko lapansi pano.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena