Deuteronomo 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Samalani, kuopera kuti mungadye ndi kukhuta, kumanga nyumba zabwino ndi kukhalamo,+ 1 Mafumu 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Solomo anatha zaka 13+ akumanga nyumba yake, ndipo anaimanga n’kuimaliza yonse.+ Salimo 49:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Zokhumba za mtima wawo n’zakuti nyumba zawo zikhalebe mpaka kalekale,+Mahema awo akhalebe ku mibadwomibadwo.+Malo awo amawatcha mayina awo.+
11 Zokhumba za mtima wawo n’zakuti nyumba zawo zikhalebe mpaka kalekale,+Mahema awo akhalebe ku mibadwomibadwo.+Malo awo amawatcha mayina awo.+