Mlaliki 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndinachita zinthu zikuluzikulu.+ Ndinadzimangira nyumba zambirimbiri.+ Ndinalima minda ya mpesa yambirimbiri.+ Mlaliki 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndinadzipangira minda yokongola ndi malo obzalamo maluwa ndi mitengo.+ Mmenemu ndinabzalamo mitengo ya zipatso zosiyanasiyana.
4 Ndinachita zinthu zikuluzikulu.+ Ndinadzimangira nyumba zambirimbiri.+ Ndinalima minda ya mpesa yambirimbiri.+
5 Ndinadzipangira minda yokongola ndi malo obzalamo maluwa ndi mitengo.+ Mmenemu ndinabzalamo mitengo ya zipatso zosiyanasiyana.